16 Dziko lawo linayambira ku Aroweli,+ mzinda umene uli m’mphepete mwa chigwa cha Arinoni, ndiponso mzinda umene uli pakati pa chigwacho. Dzikoli linaphatikizapo malo onse okwererapo apafupi ndi Medeba,+
33 Anayambira ku Yorodano chakotulukira dzuwa, dziko lonse la Giliyadi,+ Agadi,+ Arubeni+ ndi Amanase,+ kuyambira ku Aroweli+ yemwe ali pafupi ndi chigwa* cha Arinoni, ngakhalenso Giliyadi ndi Basana.+