Yeremiya 48:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwe amene ukukhala ku Aroweli, ima mʼmbali mwa msewu ndipo uone zimene zikuchitika.+ Funsa mwamuna ndi mkazi amene akuthawa kuti, ‘Chachitika nʼchiyani?’
19 Iwe amene ukukhala ku Aroweli, ima mʼmbali mwa msewu ndipo uone zimene zikuchitika.+ Funsa mwamuna ndi mkazi amene akuthawa kuti, ‘Chachitika nʼchiyani?’