Yeremiya 48:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Ima chilili ndi kuona zimene zikuchitika m’njira, iwe mkazi wokhala ku Aroweli.+ Funsa mwamuna ndi mkazi amene akuthawa. Uwafunse kuti, ‘Chachitika n’chiyani?’+
19 “Ima chilili ndi kuona zimene zikuchitika m’njira, iwe mkazi wokhala ku Aroweli.+ Funsa mwamuna ndi mkazi amene akuthawa. Uwafunse kuti, ‘Chachitika n’chiyani?’+