Numeri 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho tiyeni tiwalase.Ndithu Hesiboni adzafafanizika mpaka ku Diboni,+Amayi adzaphedwa mpaka ku Nofa, amuna mpaka ku Medeba.”+ Numeri 33:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Atanyamuka ku Iyimu anakamanga msasa ku Diboni-gadi.+ Yoswa 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Hesiboni,+ ndi midzi yake yonse+ imene inali m’malo okwererapowo. Linaphatikizaponso Diboni,+ Bamoti-baala,+ Beti-baala-meoni,+
30 Choncho tiyeni tiwalase.Ndithu Hesiboni adzafafanizika mpaka ku Diboni,+Amayi adzaphedwa mpaka ku Nofa, amuna mpaka ku Medeba.”+
17 Hesiboni,+ ndi midzi yake yonse+ imene inali m’malo okwererapowo. Linaphatikizaponso Diboni,+ Bamoti-baala,+ Beti-baala-meoni,+