Numeri 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho tiyeni tiwalase.Ndithu Hesiboni adzafafanizika mpaka ku Diboni,+Amayi adzaphedwa mpaka ku Nofa, amuna mpaka ku Medeba.”+ Numeri 32:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Tsopano ana a Gadi anayamba kumanga mizinda ya Diboni,+ Ataroti,+ Aroweli,+
30 Choncho tiyeni tiwalase.Ndithu Hesiboni adzafafanizika mpaka ku Diboni,+Amayi adzaphedwa mpaka ku Nofa, amuna mpaka ku Medeba.”+