2 Mbiri 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anamanga chipata chakumtunda+ cha nyumba ya Yehova ndipo pakhoma la Ofeli+ anamangapo zinthu zambiri. Nehemiya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda.
3 Iye anamanga chipata chakumtunda+ cha nyumba ya Yehova ndipo pakhoma la Ofeli+ anamangapo zinthu zambiri.
26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda.