Luka 1:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Mwakuti onse amene anamva anazisunga m’mitima mwawo ndi kuzisinkhasinkha.+ Iwo anali kunena kuti: “Kodi mwana ameneyu adzakhala wotani kwenikweni?” Pakuti dzanja+ la Yehova linalidi pa iye.
66 Mwakuti onse amene anamva anazisunga m’mitima mwawo ndi kuzisinkhasinkha.+ Iwo anali kunena kuti: “Kodi mwana ameneyu adzakhala wotani kwenikweni?” Pakuti dzanja+ la Yehova linalidi pa iye.