Yeremiya 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mtima wanga wasweka mkati mwanga chifukwa cha aneneri. Mafupa anga onse ayamba kunjenjemera. Ndakhala ngati munthu woledzera,+ komanso mwamuna wamphamvu amene wagonjetsedwa ndi vinyo, chifukwa cha Yehova komanso chifukwa cha mawu ake oyera.
9 Mtima wanga wasweka mkati mwanga chifukwa cha aneneri. Mafupa anga onse ayamba kunjenjemera. Ndakhala ngati munthu woledzera,+ komanso mwamuna wamphamvu amene wagonjetsedwa ndi vinyo, chifukwa cha Yehova komanso chifukwa cha mawu ake oyera.