Salimo 60:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu anu mwawaonetsa zovuta.+Mwatimwetsa vinyo ndipo tikuyenda dzandidzandi.+