Salimo 60:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwachititsa kuti anthu anu akumane ndi mavuto. Mwatimwetsa vinyo amene wachititsa kuti tiziyenda dzandidzandi.+
3 Mwachititsa kuti anthu anu akumane ndi mavuto. Mwatimwetsa vinyo amene wachititsa kuti tiziyenda dzandidzandi.+