Yesaya 44:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndine amene ndikuuza madzi akuya kuti, ‘Iphwa ndipo mitsinje yako yonse ndidzaiumitsa.’+ Yeremiya 51:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho Yehova wanena kuti: “Ine ndikukuyankhira mlandu,+ ndipo ndidzakubwezerera chilango.+ Ndidzaphwetsa nyanja yake ndi zitsime zake.+ Chivumbulutso 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mngelo wa 6+ anathira mbale yake pamtsinje waukulu wa Firate,+ ndipo madzi ake anauma,+ kuti njira ya mafumu+ ochokera kotulukira dzuwa ikonzedwe.
36 Choncho Yehova wanena kuti: “Ine ndikukuyankhira mlandu,+ ndipo ndidzakubwezerera chilango.+ Ndidzaphwetsa nyanja yake ndi zitsime zake.+
12 Mngelo wa 6+ anathira mbale yake pamtsinje waukulu wa Firate,+ ndipo madzi ake anauma,+ kuti njira ya mafumu+ ochokera kotulukira dzuwa ikonzedwe.