Yesaya 44:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndine amene ndikuuza madzi akuya kuti, ‘Iphwa ndipo mitsinje yako yonse ndidzaiumitsa.’+ Yeremiya 50:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Madzi ake adzawonongedwa ndipo adzauma.+ Dziko limeneli ndi la zifaniziro zogoba,+ ndipo anthu ake amachita zinthu mosaganiza chifukwa cha masomphenya awo ochititsa mantha.
38 Madzi ake adzawonongedwa ndipo adzauma.+ Dziko limeneli ndi la zifaniziro zogoba,+ ndipo anthu ake amachita zinthu mosaganiza chifukwa cha masomphenya awo ochititsa mantha.