Salimo 74:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndinu amene munang’amba nthaka ndi kupanga akasupe ndi makwawa.+Inu munaumitsa mitsinje imene inali kukhala ndi madzi nthawi zonse.+ Yesaya 42:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzawononga+ mapiri ndi zitunda. Ndidzaumitsa zinthu zonse zimene zinamera mmenemo. Mitsinje ndidzaisandutsa zilumba ndipo madambo ndidzawaumitsa.+ Yeremiya 50:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Madzi ake adzawonongedwa ndipo adzauma.+ Dziko limeneli ndi la zifaniziro zogoba,+ ndipo anthu ake amachita zinthu mosaganiza chifukwa cha masomphenya awo ochititsa mantha. Chivumbulutso 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mngelo wa 6+ anathira mbale yake pamtsinje waukulu wa Firate,+ ndipo madzi ake anauma,+ kuti njira ya mafumu+ ochokera kotulukira dzuwa ikonzedwe.
15 Ndinu amene munang’amba nthaka ndi kupanga akasupe ndi makwawa.+Inu munaumitsa mitsinje imene inali kukhala ndi madzi nthawi zonse.+
15 Ndidzawononga+ mapiri ndi zitunda. Ndidzaumitsa zinthu zonse zimene zinamera mmenemo. Mitsinje ndidzaisandutsa zilumba ndipo madambo ndidzawaumitsa.+
38 Madzi ake adzawonongedwa ndipo adzauma.+ Dziko limeneli ndi la zifaniziro zogoba,+ ndipo anthu ake amachita zinthu mosaganiza chifukwa cha masomphenya awo ochititsa mantha.
12 Mngelo wa 6+ anathira mbale yake pamtsinje waukulu wa Firate,+ ndipo madzi ake anauma,+ kuti njira ya mafumu+ ochokera kotulukira dzuwa ikonzedwe.