Salimo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dziko lapansi linayamba kugwedezekera uku ndi uku ndiponso kutekeseka.+Maziko a mapiri anagwedezeka,+Anagwedezekera uku ndi uku chifukwa Mulungu anakwiya.+ Yeremiya 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndinaona mapiri ndipo anali kugwedezeka. Zitunda zonse zinali kunjenjemera.+ Zefaniya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsiku limenelo ndi tsiku lamkwiyo, tsiku lansautso ndi zowawa,+ tsiku la mphepo yamkuntho ndi losakaza, tsiku lamdima wochititsa mantha,+ tsiku lamitambo yakuda ndi lamdima wandiweyani.
7 Dziko lapansi linayamba kugwedezekera uku ndi uku ndiponso kutekeseka.+Maziko a mapiri anagwedezeka,+Anagwedezekera uku ndi uku chifukwa Mulungu anakwiya.+
15 Tsiku limenelo ndi tsiku lamkwiyo, tsiku lansautso ndi zowawa,+ tsiku la mphepo yamkuntho ndi losakaza, tsiku lamdima wochititsa mantha,+ tsiku lamitambo yakuda ndi lamdima wandiweyani.