Salimo 77:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+ Salimo 97:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mphezi zake zinawalitsa dziko lapansi.+Dziko linaona ndipo linachita mantha kwambiri.+ Chivumbulutso 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo kunachitika mphezi, kunamveka mawu, ndipo kunagunda mabingu. Kunachitanso chivomezi chachikulu+ chimene sichinachitikepo chikhalire anthu padziko lapansi,+ chivomezi+ champhamvu kwambiri, chachikulu zedi.
18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+
18 Pamenepo kunachitika mphezi, kunamveka mawu, ndipo kunagunda mabingu. Kunachitanso chivomezi chachikulu+ chimene sichinachitikepo chikhalire anthu padziko lapansi,+ chivomezi+ champhamvu kwambiri, chachikulu zedi.