Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 77:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Madzi akuonani, inu Mulungu,

      Madzi akuonani, ndipo ayamba kumva ululu woopsa.+

      Komanso madzi akuya ayamba kuwinduka.+

  • Salimo 104:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Amayang’ana dziko lapansi ndipo limanjenjemera.+

      Amagwira mapiri ndipo amafuka utsi.+

  • Salimo 114:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Chifukwa cha Ambuye, chita mantha aakulu dziko lapansi iwe,+

      Chita mantha aakulu chifukwa cha Mulungu wa Yakobo,

  • Yeremiya 51:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Dziko ligwedezeke ndi kumva ululu waukulu,+ chifukwa Yehova waganiza zokhaulitsa Babulo kuti dzikolo likhale chinthu chodabwitsa, lopanda munthu wokhalamo.+

  • Habakuku 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mapiri anakuonani ndipo anamva ululu waukulu.+ Mvula yamphamvu yamabingu inadutsa. Madzi akuya anachita mkokomo+ ndipo anathuvuka m’malere.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena