Salimo 97:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mphezi zake zinawalitsa dziko lapansi.+Dziko linaona ndipo linachita mantha kwambiri.+ Habakuku 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuwala kwake kunali ngati kuwala kwa masana.+ Kuwala kwa mitundu iwiri kunali kutuluka m’dzanja lake ndipo m’dzanja lakemo ndi mmene munali kubisala mphamvu zake.+
4 Kuwala kwake kunali ngati kuwala kwa masana.+ Kuwala kwa mitundu iwiri kunali kutuluka m’dzanja lake ndipo m’dzanja lakemo ndi mmene munali kubisala mphamvu zake.+