Ekisodo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+ Yobu 36:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Iye wafumbata mphezi m’manja mwake,Ndipo amailamula kuti igwere woukira.+ Salimo 77:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+ Salimo 144:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ng’animitsani mphezi kuti muwabalalitse.+Tumizani mivi yanu kuti muwasokoneze.+
18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+
18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+