2 Samueli 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anayamba kuponya mivi kuti awabalalitse.+Anaponya mphezi kuti awasokoneze.+ Yobu 36:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Iye wafumbata mphezi m’manja mwake,Ndipo amailamula kuti igwere woukira.+ Salimo 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anayamba kuponya mivi kuti awabalalitse.+Anaponya mphezi kuti awasokoneze.+ Salimo 77:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+ Salimo 97:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mphezi zake zinawalitsa dziko lapansi.+Dziko linaona ndipo linachita mantha kwambiri.+ Zekariya 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zidzakhala zoonekeratu kuti Yehova ali ndi anthu ake,+ ndipo muvi wake udzathamanga ngati mphezi.+ Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa adzaliza lipenga lanyanga ya nkhosa,+ ndipo adzapita ndi mphepo yamkuntho ya kum’mwera.+
18 Phokoso la bingu lanu linali ngati la mawilo a galeta.+Mphezi zinaunika padziko.+Ndipo dziko lapansi linagwedezeka ndi kuyamba kunjenjemera.+
14 Zidzakhala zoonekeratu kuti Yehova ali ndi anthu ake,+ ndipo muvi wake udzathamanga ngati mphezi.+ Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa adzaliza lipenga lanyanga ya nkhosa,+ ndipo adzapita ndi mphepo yamkuntho ya kum’mwera.+