Yoswa 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ansembewo akadzaliza malipenga a nyanga za nkhosa, ndipo inu mukadzamva kulira kwa malipengawo, nonse mudzafuule mfuu yankhondo mwamphamvu,+ ndipo mpanda wonse wa mzindawo udzagwa pansi.+ Pamenepo, nonsenu mudzathamangire kumeneko.” Yesaya 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu nonse okhala panthaka ndi inu okhala m’dziko lapansi,+ mudzaona chinthu chooneka ngati chizindikiro chimene chimaikidwa pamapiri,+ ndipo mudzamva zofanana ndi kulira kwa lipenga.+
5 Ansembewo akadzaliza malipenga a nyanga za nkhosa, ndipo inu mukadzamva kulira kwa malipengawo, nonse mudzafuule mfuu yankhondo mwamphamvu,+ ndipo mpanda wonse wa mzindawo udzagwa pansi.+ Pamenepo, nonsenu mudzathamangire kumeneko.”
3 Inu nonse okhala panthaka ndi inu okhala m’dziko lapansi,+ mudzaona chinthu chooneka ngati chizindikiro chimene chimaikidwa pamapiri,+ ndipo mudzamva zofanana ndi kulira kwa lipenga.+