Yesaya 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye waikira chizindikiro mtundu waukulu wakutali.+ Wauimbira likhweru kumapeto kwa dziko lapansi.+ Ndipotu mtunduwo udzachita changu n’kubwera msangamsanga.+ Yesaya 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Amuna inu, imikani chizindikiro+ paphiri la miyala yokhayokha. Afuulireni! Akodoleni ndi dzanja,+ kuti adzalowe pamakomo a anthu olemekezeka.+
26 Iye waikira chizindikiro mtundu waukulu wakutali.+ Wauimbira likhweru kumapeto kwa dziko lapansi.+ Ndipotu mtunduwo udzachita changu n’kubwera msangamsanga.+
2 “Amuna inu, imikani chizindikiro+ paphiri la miyala yokhayokha. Afuulireni! Akodoleni ndi dzanja,+ kuti adzalowe pamakomo a anthu olemekezeka.+