Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 50:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Nenani ndi kulengeza zimene zachitika kwa anthu a mitundu ina.+ Imikani mtengo wachizindikiro+ ndipo lengezani zimenezi. Musabise kalikonse amuna inu. Nenani kuti, ‘Babulo walandidwa.+ Beli wachititsidwa manyazi.+ Merodake wachita mantha. Mafano a Babulo achita manyazi.+ Mafano ake onyansawo* achita mantha.’

  • Yeremiya 51:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kwezerani mpanda wa Babulo mtengo wa chizindikiro.+ Wonjezerani alonda+ ndipo ikani alondawo pamalo awo. Konzekeretsani omenya nkhondo mobisalira anzawo.+ Pakuti Yehova waganiza zoti achite ndipo adzachitira anthu okhala ku Babulo zimene wanena.”+

  • Yeremiya 51:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Kwezani mtengo wa chizindikiro amuna inu.+ Imbani lipenga pakati pa mitundu ya anthu. Konzekeretsani+ mitundu ya anthu yoti imuthire nkhondo. Muitanireni maufumu a ku Ararati,+ ku Mini ndi ku Asikenazi.+ Muikireni wolemba anthu usilikali. Mubweretsereni mahatchi+ ngati dzombe lokhala ndi ubweya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena