Yesaya 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Beli+ wawerama+ ndipo Nebo wagwada. Mafano awo+ akhala katundu wa nyama zakutchire ndi wa nyama zoweta. Mafanowo angokhala katundu wolemera kwa nyama zotopa. Yeremiya 51:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndidzalanga Beli+ ku Babulo ndipo ndidzamulavulitsa zimene wameza.+ Mitundu ya anthu sidzakhamukiranso kwa iye.+ Kuwonjezera apo, mpanda wa Babulo udzagwa.+
46 Beli+ wawerama+ ndipo Nebo wagwada. Mafano awo+ akhala katundu wa nyama zakutchire ndi wa nyama zoweta. Mafanowo angokhala katundu wolemera kwa nyama zotopa.
44 Ndidzalanga Beli+ ku Babulo ndipo ndidzamulavulitsa zimene wameza.+ Mitundu ya anthu sidzakhamukiranso kwa iye.+ Kuwonjezera apo, mpanda wa Babulo udzagwa.+