Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 50:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Iwe Babulo ndinakutchera msampha ndipo wakodwa koma iwe sunadziwe.+ Unapezeka ndi kugwidwa chifukwa unali kulimbana ndi Yehova.+

  • Yeremiya 50:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha phokoso la kugwidwa kwa Babulo,+ ndipo kulira kudzamveka pakati pa mitundu ya anthu.”+

  • Yeremiya 51:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Babulo wagwa mwadzidzidzi moti wasweka.+ Mulireni mofuula anthu inu.+ M’patseni mafuta a basamu kuti muthetse ululu wake,+ mwina achira.”

  • Chivumbulutso 14:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kenako mngelo wina wachiwiri anamutsatira, ndipo anati: “Wagwa! Babulo+ Wamkulu wagwa,+ amene anachititsa mitundu yonse ya anthu kumwako vinyo+ wa mkwiyo wake ndi wa dama* lake!”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena