Yesaya 37:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atentha milungu yawo pamoto,+ chifukwa sinali milungu,+ koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala, n’chifukwa chake anaiwononga.+ Zefaniya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzawachititsa mantha,+ pakuti adzawondetsa milungu yonse ya padziko lapansi.+ Pamenepo anthu adzamugwadira,+ aliyense pamalo pake, zilumba zonse za mitundu ya anthu zidzamugwadira.+
19 Atentha milungu yawo pamoto,+ chifukwa sinali milungu,+ koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala, n’chifukwa chake anaiwononga.+
11 Yehova adzawachititsa mantha,+ pakuti adzawondetsa milungu yonse ya padziko lapansi.+ Pamenepo anthu adzamugwadira,+ aliyense pamalo pake, zilumba zonse za mitundu ya anthu zidzamugwadira.+