Yesaya 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Amuna inu, imikani chizindikiro+ paphiri la miyala yokhayokha. Afuulireni! Akodoleni ndi dzanja,+ kuti adzalowe pamakomo a anthu olemekezeka.+
2 “Amuna inu, imikani chizindikiro+ paphiri la miyala yokhayokha. Afuulireni! Akodoleni ndi dzanja,+ kuti adzalowe pamakomo a anthu olemekezeka.+