Yeremiya 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mufuulireni mfuu yankhondo kuchokera kumbali zonse.+ Wagwetsa manja ake+ ndipo zipilala zake zagwa. Mipanda yake yagwetsedwa,+ pakuti Yehova akumubwezera.+ Mubwezereni, ndipo monga mmene iye anachitira, inunso muchitireni zomwezo.+ Hoseya 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Lizani lipenga la nyanga ya nkhosa+ ku Gibeya!+ Lizani lipenga ku Rama! Fuulani mfuu ya nkhondo ku Beti-aveni!+ Tili pambuyo pako, iwe Benjamini!+
15 Mufuulireni mfuu yankhondo kuchokera kumbali zonse.+ Wagwetsa manja ake+ ndipo zipilala zake zagwa. Mipanda yake yagwetsedwa,+ pakuti Yehova akumubwezera.+ Mubwezereni, ndipo monga mmene iye anachitira, inunso muchitireni zomwezo.+
8 “Lizani lipenga la nyanga ya nkhosa+ ku Gibeya!+ Lizani lipenga ku Rama! Fuulani mfuu ya nkhondo ku Beti-aveni!+ Tili pambuyo pako, iwe Benjamini!+