-
Yeremiya 51:58Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
58 Yehova wa makamu wanena kuti: “Ngakhale kuti mpanda wa Babulo ndi waukulu udzagwetsedwa ndithu.+ Ngakhale kuti zipata zake ndi zazitali zidzatenthedwa.+ Anthu adzagwira ntchito yolemetsa pachabe.+ Mitundu ya anthu idzagwira ntchito yolemetsa imene idzawonongedwa ndi moto+ ndipo adzangodzitopetsa.”
-