Yeremiya 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mufuulireni mfuu yankhondo kuchokera kumbali zonse.+ Wagwetsa manja ake+ ndipo zipilala zake zagwa. Mipanda yake yagwetsedwa,+ pakuti Yehova akumubwezera.+ Mubwezereni, ndipo monga mmene iye anachitira, inunso muchitireni zomwezo.+ Yeremiya 51:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndidzalanga Beli+ ku Babulo ndipo ndidzamulavulitsa zimene wameza.+ Mitundu ya anthu sidzakhamukiranso kwa iye.+ Kuwonjezera apo, mpanda wa Babulo udzagwa.+
15 Mufuulireni mfuu yankhondo kuchokera kumbali zonse.+ Wagwetsa manja ake+ ndipo zipilala zake zagwa. Mipanda yake yagwetsedwa,+ pakuti Yehova akumubwezera.+ Mubwezereni, ndipo monga mmene iye anachitira, inunso muchitireni zomwezo.+
44 Ndidzalanga Beli+ ku Babulo ndipo ndidzamulavulitsa zimene wameza.+ Mitundu ya anthu sidzakhamukiranso kwa iye.+ Kuwonjezera apo, mpanda wa Babulo udzagwa.+