Yeremiya 51:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova wa makamu walumbira m’dzina lake+ kuti, ‘M’dziko lako ndidzadzazamo amuna ngati dzombe+ ndipo amunawo adzaimba mokondwa chifukwa chokugonjetsa.’+ Yeremiya 51:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ine ndikuthira nkhondo iwe+ phiri lowononga,+ amene wawononga dziko lonse lapansi.+ Ndidzatambasula dzanja langa ndi kukuthira nkhondo. Ndidzakugubuduza kukuchotsa pamatanthwe ndipo ndidzakusandutsa phiri lotenthedwa ndi moto,” watero Yehova.+
14 Yehova wa makamu walumbira m’dzina lake+ kuti, ‘M’dziko lako ndidzadzazamo amuna ngati dzombe+ ndipo amunawo adzaimba mokondwa chifukwa chokugonjetsa.’+
25 “Ine ndikuthira nkhondo iwe+ phiri lowononga,+ amene wawononga dziko lonse lapansi.+ Ndidzatambasula dzanja langa ndi kukuthira nkhondo. Ndidzakugubuduza kukuchotsa pamatanthwe ndipo ndidzakusandutsa phiri lotenthedwa ndi moto,” watero Yehova.+