Yeremiya 50:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Taona! Iwe Babulo Wodzikuza,+ ndikukuthira nkhondo,”+ watero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa.+ “Pakuti tsiku lako lifika, nthawi imene ndiyenera kukulanga.
31 “Taona! Iwe Babulo Wodzikuza,+ ndikukuthira nkhondo,”+ watero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa.+ “Pakuti tsiku lako lifika, nthawi imene ndiyenera kukulanga.