Habakuku 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Taona! Kodi si Yehova wa makamu amene adzachititsa anthu kugwira ntchito yakalavulagaga kuti moto uwononge ntchitoyo? Kodi sindiye amene wachititsa kuti mitundu ya anthu idzitopetse pachabe?+
13 Taona! Kodi si Yehova wa makamu amene adzachititsa anthu kugwira ntchito yakalavulagaga kuti moto uwononge ntchitoyo? Kodi sindiye amene wachititsa kuti mitundu ya anthu idzitopetse pachabe?+