Habakuku 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Taona! Kodi si Yehova wa magulu ankhondo akumwamba amene adzachititse anthu kugwira ntchito mwakhama kuti moto uwononge ntchitoyo?Ndiponso kuti mitundu ya anthu idzitopetse pachabe?+ Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:13 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 17
13 Taona! Kodi si Yehova wa magulu ankhondo akumwamba amene adzachititse anthu kugwira ntchito mwakhama kuti moto uwononge ntchitoyo?Ndiponso kuti mitundu ya anthu idzitopetse pachabe?+