Habakuku 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Taona! Kodi si Yehova wa makamu amene adzachititsa anthu kugwira ntchito yakalavulagaga kuti moto uwononge ntchitoyo? Kodi sindiye amene wachititsa kuti mitundu ya anthu idzitopetse pachabe?+ Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:13 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 17
13 Taona! Kodi si Yehova wa makamu amene adzachititsa anthu kugwira ntchito yakalavulagaga kuti moto uwononge ntchitoyo? Kodi sindiye amene wachititsa kuti mitundu ya anthu idzitopetse pachabe?+