Yeremiya 51:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Amuna amphamvu a ku Babulo asiya kumenya nkhondo. Iwo angokhala m’malo otetezeka. Mphamvu zawo zatha.+ Akhala ngati akazi.+ Nyumba za m’Babulo zatenthedwa. Mipiringidzo yake yathyoledwa.+
30 “Amuna amphamvu a ku Babulo asiya kumenya nkhondo. Iwo angokhala m’malo otetezeka. Mphamvu zawo zatha.+ Akhala ngati akazi.+ Nyumba za m’Babulo zatenthedwa. Mipiringidzo yake yathyoledwa.+