Yesaya 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’tsiku limenelo, Aiguputo adzakhala ngati akazi. Iwo adzanjenjemera+ ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa makamu adzawatambasulira dzanja lake.+ Yeremiya 50:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Lupanga lidzawononga mahatchi awo,+ magaleta awo ankhondo ndi khamu lonse la anthu a mitundu yosiyanasiyana amene ali pakati pawo+ ndipo adzakhala ngati akazi.+ Lupanga lidzawononga chuma chake+ ndipo chidzafunkhidwa.
16 M’tsiku limenelo, Aiguputo adzakhala ngati akazi. Iwo adzanjenjemera+ ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa makamu adzawatambasulira dzanja lake.+
37 Lupanga lidzawononga mahatchi awo,+ magaleta awo ankhondo ndi khamu lonse la anthu a mitundu yosiyanasiyana amene ali pakati pawo+ ndipo adzakhala ngati akazi.+ Lupanga lidzawononga chuma chake+ ndipo chidzafunkhidwa.