Salimo 48:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumeneko iwo anayamba kunjenjemera,+Anamva zopweteka ngati za mkazi amene akubereka.+ Yeremiya 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu, funsani kuti mudziwe ngati mwamuna angabale mwana.+ N’chifukwa chiyani mwamuna aliyense wamphamvu akuoneka atagwira manja m’chiuno ngati mkazi amene akubala mwana? N’chifukwa chiyani nkhope zawo zonse zafooka?+
6 Anthu inu, funsani kuti mudziwe ngati mwamuna angabale mwana.+ N’chifukwa chiyani mwamuna aliyense wamphamvu akuoneka atagwira manja m’chiuno ngati mkazi amene akubala mwana? N’chifukwa chiyani nkhope zawo zonse zafooka?+