Yesaya 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa tsiku limenelo Aiguputo adzakhala ngati akazi ndipo adzanjenjemera ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzatambasula dzanja loopsa kuti awapatse chilango.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:16 Yesaya 1, ptsa. 203-204
16 Pa tsiku limenelo Aiguputo adzakhala ngati akazi ndipo adzanjenjemera ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzatambasula dzanja loopsa kuti awapatse chilango.+