Yesaya 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’tsiku limenelo, Aiguputo adzakhala ngati akazi. Iwo adzanjenjemera+ ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa makamu adzawatambasulira dzanja lake.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:16 Yesaya 1, ptsa. 203-204
16 M’tsiku limenelo, Aiguputo adzakhala ngati akazi. Iwo adzanjenjemera+ ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa makamu adzawatambasulira dzanja lake.+