Yeremiya 51:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kudzera mwa iwe ndidzaphwanya hatchi ndi wokwerapo wake kukhala zidutswazidutswa. Kudzera mwa iwe ndidzaphwanya magaleta* ankhondo ndi okweramo ake kukhala zidutswazidutswa.+
21 Kudzera mwa iwe ndidzaphwanya hatchi ndi wokwerapo wake kukhala zidutswazidutswa. Kudzera mwa iwe ndidzaphwanya magaleta* ankhondo ndi okweramo ake kukhala zidutswazidutswa.+