Oweruza 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amene anali m’chigwa anachokera m’fuko la Efuraimu,+Ndipo iwo anali ndi iwe Benjamini, pakati pa anthu a mtundu wako.Atsogoleri a asilikali anachokera kwa Makiri,+Ndipo osunga zida za mlembi, anachokera m’fuko la Zebuloni.+
14 Amene anali m’chigwa anachokera m’fuko la Efuraimu,+Ndipo iwo anali ndi iwe Benjamini, pakati pa anthu a mtundu wako.Atsogoleri a asilikali anachokera kwa Makiri,+Ndipo osunga zida za mlembi, anachokera m’fuko la Zebuloni.+