Yeremiya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nenani zimenezi mu Yuda anthu inu, ndipo zilengezeni ngakhale mu Yerusalemu.+ Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa m’dziko lonse.+ Fuulani kuti: “Sonkhanani pamodzi, ndipo tiyeni tilowe m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Hoseya 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ika lipenga la nyanga ya nkhosa pakamwa pako ndipo ulilize.+ Mdani akubwera ngati chiwombankhanga+ kudzaukira nyumba ya Yehova. Akubwera chifukwa Aisiraeli aphwanya pangano langa+ ndiponso aphwanya malamulo anga.+ Yoweli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lizani lipenga m’Ziyoni+ amuna inu ndipo fuulani mfuu yankhondo+ m’phiri langa loyera.+ Anthu onse okhala m’dzikoli anjenjemere,+ pakuti tsiku la Yehova likubwera+ ndipo lili pafupi!
5 Nenani zimenezi mu Yuda anthu inu, ndipo zilengezeni ngakhale mu Yerusalemu.+ Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa m’dziko lonse.+ Fuulani kuti: “Sonkhanani pamodzi, ndipo tiyeni tilowe m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+
8 “Ika lipenga la nyanga ya nkhosa pakamwa pako ndipo ulilize.+ Mdani akubwera ngati chiwombankhanga+ kudzaukira nyumba ya Yehova. Akubwera chifukwa Aisiraeli aphwanya pangano langa+ ndiponso aphwanya malamulo anga.+
2 “Lizani lipenga m’Ziyoni+ amuna inu ndipo fuulani mfuu yankhondo+ m’phiri langa loyera.+ Anthu onse okhala m’dzikoli anjenjemere,+ pakuti tsiku la Yehova likubwera+ ndipo lili pafupi!