Yeremiya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nenani zimenezi mu Yuda anthu inu, ndipo zilengezeni ngakhale mu Yerusalemu.+ Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa m’dziko lonse.+ Fuulani kuti: “Sonkhanani pamodzi, ndipo tiyeni tilowe m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Ezekieli 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 mlondayo akaona lupanga likubwera m’dzikomo iye n’kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa kuchenjeza anthu,+
5 Nenani zimenezi mu Yuda anthu inu, ndipo zilengezeni ngakhale mu Yerusalemu.+ Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa m’dziko lonse.+ Fuulani kuti: “Sonkhanani pamodzi, ndipo tiyeni tilowe m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+
3 mlondayo akaona lupanga likubwera m’dzikomo iye n’kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa kuchenjeza anthu,+