Yoweli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lizani lipenga mu Ziyoni.+ Lengezani mʼphiri langa loyera kuti kukubwera nkhondo. Anthu onse okhala mʼdzikoli anjenjemere,Chifukwa tsiku la Yehova likubwera+ ndipo lili pafupi.
2 “Lizani lipenga mu Ziyoni.+ Lengezani mʼphiri langa loyera kuti kukubwera nkhondo. Anthu onse okhala mʼdzikoli anjenjemere,Chifukwa tsiku la Yehova likubwera+ ndipo lili pafupi.