Yoweli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lizani lipenga m’Ziyoni+ amuna inu ndipo fuulani mfuu yankhondo+ m’phiri langa loyera.+ Anthu onse okhala m’dzikoli anjenjemere,+ pakuti tsiku la Yehova likubwera+ ndipo lili pafupi! Amosi 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lipenga la nyanga ya nkhosa likalira mumzinda, kodi anthu sanjenjemera?+ Kodi tsoka likagwa mumzinda si Yehova amene wachititsa? Zekariya 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zidzakhala zoonekeratu kuti Yehova ali ndi anthu ake,+ ndipo muvi wake udzathamanga ngati mphezi.+ Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa adzaliza lipenga lanyanga ya nkhosa,+ ndipo adzapita ndi mphepo yamkuntho ya kum’mwera.+
2 “Lizani lipenga m’Ziyoni+ amuna inu ndipo fuulani mfuu yankhondo+ m’phiri langa loyera.+ Anthu onse okhala m’dzikoli anjenjemere,+ pakuti tsiku la Yehova likubwera+ ndipo lili pafupi!
6 Lipenga la nyanga ya nkhosa likalira mumzinda, kodi anthu sanjenjemera?+ Kodi tsoka likagwa mumzinda si Yehova amene wachititsa?
14 Zidzakhala zoonekeratu kuti Yehova ali ndi anthu ake,+ ndipo muvi wake udzathamanga ngati mphezi.+ Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa adzaliza lipenga lanyanga ya nkhosa,+ ndipo adzapita ndi mphepo yamkuntho ya kum’mwera.+