Yesaya 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Uwu ndi uthenga wokhudza chipululu cha nyanja:*+ Kuchipululu kukubwera chinthu chinachake kuchokera kudziko lochititsa mantha.+ Chikubwera ngati mphepo yamkuntho+ yochokera kum’mwera. Yesaya 66:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Pakuti Yehova akubwera ngati moto,+ ndipo magaleta ake ali ngati mphepo yamkuntho+ kuti adzawabwezere mwaukali ndi mokwiya, ndiponso kuti adzawadzudzule ndi malawi a moto.+
21 Uwu ndi uthenga wokhudza chipululu cha nyanja:*+ Kuchipululu kukubwera chinthu chinachake kuchokera kudziko lochititsa mantha.+ Chikubwera ngati mphepo yamkuntho+ yochokera kum’mwera.
15 “Pakuti Yehova akubwera ngati moto,+ ndipo magaleta ake ali ngati mphepo yamkuntho+ kuti adzawabwezere mwaukali ndi mokwiya, ndiponso kuti adzawadzudzule ndi malawi a moto.+