Yesaya 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uwu ndi uthenga wokhudza Babulo,+ umene Yesaya mwana wa Amozi+ anaona m’masomphenya: Yesaya 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’Babulo simudzakhalanso anthu,+ ndipo iye sadzakhalaponso ku mibadwomibadwo.+ Kumeneko Mluya sadzakhomako hema wake, ndipo abusa sadzagonekako ziweto zawo. Yeremiya 51:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Nyanja yasefukira ndi kumiza Babulo. Mzinda wa Babulo wamizidwa pansi pa mafunde ambiri a nyanjayo.+
20 M’Babulo simudzakhalanso anthu,+ ndipo iye sadzakhalaponso ku mibadwomibadwo.+ Kumeneko Mluya sadzakhomako hema wake, ndipo abusa sadzagonekako ziweto zawo.
42 Nyanja yasefukira ndi kumiza Babulo. Mzinda wa Babulo wamizidwa pansi pa mafunde ambiri a nyanjayo.+