Salimo 50:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu wathu adzabwera ndipo sadzakhala chete.+Pamaso pake pali moto wonyeketsa,+Ndipo pamalo onse omuzungulira pali mkuntho wamphamvu.+ Yeremiya 25:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Taonani! Tsoka likuyenda kuchokera mu mtundu wina kupita mu mtundu wina,+ ndipo mkuntho wamphamvu udzafika kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+
3 Mulungu wathu adzabwera ndipo sadzakhala chete.+Pamaso pake pali moto wonyeketsa,+Ndipo pamalo onse omuzungulira pali mkuntho wamphamvu.+
32 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Taonani! Tsoka likuyenda kuchokera mu mtundu wina kupita mu mtundu wina,+ ndipo mkuntho wamphamvu udzafika kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+