Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 30:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+

  • Yesaya 66:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Pakuti Yehova akubwera ngati moto,+ ndipo magaleta ake ali ngati mphepo yamkuntho+ kuti adzawabwezere mwaukali ndi mokwiya, ndiponso kuti adzawadzudzule ndi malawi a moto.+

  • Yeremiya 23:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Taonani! Mphepo yamkuntho yochokera kwa Yehova idzawomba. Mkwiyo wake udzawomba ngati kamvulumvulu wamphamvu.+ Udzawomba pamitu ya anthu oipawo.+

  • Yeremiya 30:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Taonani! Mphepo yamkuntho yochokera kwa Yehova yawomba. Mkwiyo wake wawomba ngati kamvulumvulu wosakaza.+ Wawomba pamitu ya anthu oipa.+

  • Zefaniya 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “‘Choncho pitirizani kundiyembekezera,’+ watero Yehova, ‘mpaka tsiku limene ndidzanyamuka kuti ndikaukire ndi kulanda zinthu zofunkhidwa.+ Chigamulo changa ndicho kusonkhanitsa mitundu ya anthu+ ndi kusonkhanitsa pamodzi maufumu kuti ndiwadzudzule mwamphamvu+ ndi kuwatsanulira mkwiyo wanga wonse woyaka moto, pakuti moto wa mkwiyo wanga udzanyeketsa dziko lonse lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena