Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 9:57
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 57 Ndipo zoipa zonse za amuna a m’Sekemu, Mulungu anachititsa kuti ziwabwerere pamutu pawo, kuti temberero+ la Yotamu+ mwana wa Yerubaala,+ liwagwere.+

  • 1 Samueli 25:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ndiyeno Davide anamva kuti Nabala wamwalira. Atatero, iye anati: “Adalitsike Yehova amene wandiweruzira mlandu+ ndi kundimasula ku chitonzo+ cha Nabala, komanso wagwira ine mtumiki wake kuti ndisachite choipa.+ Yehova wabwezera zoipa za Nabala pamutu pake!”+ Pamenepo Davide anatumiza anthu kuti akamufunsirire Abigayeli, kuti akhale mkazi wake.+

  • Nehemiya 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Nehemiya anati: “Inu Mulungu wathu, imvani+ mawu onyoza amene akutinenera.+ Bwezerani chitonzo chawocho+ pamutu pawo ndipo apititseni m’dziko laukapolo monga zofunkha.

  • Yeremiya 30:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Taonani! Mphepo yamkuntho yochokera kwa Yehova yawomba. Mkwiyo wake wawomba ngati kamvulumvulu wosakaza.+ Wawomba pamitu ya anthu oipa.+

  • Yoweli 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 tsopano ndiwatenga kuti achoke kumalo amene munawagulitsa+ ndipo ndikubwezerani zimene munachita.+

  • Obadiya 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsiku la Yehova limene adzawononge mitundu yonse ya anthu lili pafupi.+ Iwe adzakuchitira zofanana ndi zimene wachitira m’bale wako.+ Zimene unachita zidzabwerera pamutu pako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena